Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+

  • Yoswa 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo mayiyo anatenga amuna awiriwo n’kuwabisa. Kenako anayankha kuti: “Inde, amunawo anabweradi kwa ine, koma sindinadziwe kuti achokera kuti.

  • Yoswa 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 (Koma iye anali atawatengera padenga,*+ ndi kuwabisa pansi pa mapesi a fulakesi* padengapo.)

  • Mateyu 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+

  • Aheberi 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.

  • Yakobo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 N’chimodzimodzinso ndi Rahabi.+ Kodi Rahabi hule lija, silinaonedwe ngati lolungama chifukwa cha ntchito zake, powalandira bwino azondi aja ndi kuwabweza kwawo powasonyeza njira ina?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena