Luka 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+ Chivumbulutso 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwowa adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma pakuti iye ndiye Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+
38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+
14 Iwowa adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma pakuti iye ndiye Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+