Mateyu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi. Machitidwe 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.” 1 Timoteyo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wachimwemwe ndi Wamphamvu yekhayo,+ iye amene ali Mfumu+ ya olamulira monga mafumu ndi Mbuye+ wa olamulira monga ambuye, adzaonekera pa nthawi zake zoikidwiratu.+
18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.
36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.”
15 Wachimwemwe ndi Wamphamvu yekhayo,+ iye amene ali Mfumu+ ya olamulira monga mafumu ndi Mbuye+ wa olamulira monga ambuye, adzaonekera pa nthawi zake zoikidwiratu.+