Yohane 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+ Machitidwe 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.
6 Koma pamene ansembe aakulu ndi alonda anamuona, anafuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+ Pilato anawauza kuti: “M’tengeni mukamupachike nokha, chifukwa ine sindikupeza mlandu uliwonse mwa iye.”+
10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.