Machitidwe 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.”
36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu, kuti Yesu ameneyu, amene inu munam’pachika,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.”