Ekisodo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+ Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+ Maliko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo iwo anafuula kuti: “M’pachikeni!”+ Luka 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo anthuwo anayamba kufuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+
7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+