Luka 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo ankanena kuti: “Wodalitsidwa ndi amene akubwera monga Mfumu mʼdzina la Yehova!* Mtendere kumwamba ndi ulemerero kumwambamwambako!”+
38 Iwo ankanena kuti: “Wodalitsidwa ndi amene akubwera monga Mfumu mʼdzina la Yehova!* Mtendere kumwamba ndi ulemerero kumwambamwambako!”+