Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 22:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.

  • 2 Samueli 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno tsiku lina madzulo, Davide anadzuka pabedi lake, n’kupita kukayendayenda padenga*+ la nyumba yachifumu. Ali pamenepo anaona+ mkazi akusamba, ndipo mkaziyo anali wooneka bwino kwambiri.+

  • Machitidwe 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena