Deuteronomo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukamanga nyumba yatsopano muzimanganso kampanda padenga la nyumbayo+ kuopera kuti nyumba yanu ingakhale ndi mlandu wa magazi ngati munthu atagwa kuchokera padengapo. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:8 Nsanja ya Olonda,4/1/2013, tsa. 102/1/2001, ptsa. 4-5
8 Mukamanga nyumba yatsopano muzimanganso kampanda padenga la nyumbayo+ kuopera kuti nyumba yanu ingakhale ndi mlandu wa magazi ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.