Deuteronomo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:8 Nsanja ya Olonda,4/1/2013, tsa. 102/1/2001, ptsa. 4-5
8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.