2 Samueli 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku lina madzulo, Davide anadzuka pabedi lake, n’kupita kukayendayenda padenga*+ la nyumba yachifumu. Ali pamenepo anaona+ mkazi akusamba, ndipo mkaziyo anali wooneka bwino kwambiri.+ Machitidwe 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+
2 Ndiyeno tsiku lina madzulo, Davide anadzuka pabedi lake, n’kupita kukayendayenda padenga*+ la nyumba yachifumu. Ali pamenepo anaona+ mkazi akusamba, ndipo mkaziyo anali wooneka bwino kwambiri.+
9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+