-
1 Samueli 9:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno Samueli ndi Sauli anadzuka m’mawa kwambiri, m’bandakucha, ndipo Samueli, ali padenga la nyumba, anaitana Sauli ndi kumuuza kuti: “Konzekera ulendo.” Pamenepo Sauli ananyamuka ndipo onse awiri, iyeyo ndi Samueli, anatuluka kupita panja.
-