Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+ Salimo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.+Dzanja lanu lamanja lidzapeza odana nanu.
29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+