Numeri 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aisiraeli ataona zimenezo, analonjeza kwa Yehova kuti:+ “Mukapereka anthuwa m’manja mwathu, ndithu ifenso tidzawononga mizinda yawo.”+ 1 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa,+ Aamaleki, ndi kumenyana nawo kufikira utawafafaniza.’+
2 Aisiraeli ataona zimenezo, analonjeza kwa Yehova kuti:+ “Mukapereka anthuwa m’manja mwathu, ndithu ifenso tidzawononga mizinda yawo.”+
18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa,+ Aamaleki, ndi kumenyana nawo kufikira utawafafaniza.’+