1 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa, Aamaleki.+ Ukamenyane nawo mpaka ukawaphe onse.’+
18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa, Aamaleki.+ Ukamenyane nawo mpaka ukawaphe onse.’+