Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “‘Ngati munthu watenga munthu mnzake, nyama kapena munda wake n’kuupatula kuti ukhale woyera kwa Yehova kwamuyaya,* kapena akapereka munthuyo, nyama kapena munda kwa Mulungu kuti auwononge,+ sungagulitsidwe kapena kuwomboledwa.+ Munthu, nyama kapena munda umenewo ndi wopatulika koposa. Zimenezi ndi za Yehova.

  • Numeri 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova anamva mawu a Aisiraeli, ndipo anapereka Akananiwo m’manja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. N’chifukwa chake malowo anawatcha Horima.*+

  • Deuteronomo 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+

  • Deuteronomo 20:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena