-
Mateyu 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Salimoni anabereka Boazi, ndipo mayi ake anali Rahabi.+
Boazi anabereka Obedi, ndipo mayi ake anali Rute.+
Obedi anabereka Jese.+
-