Aheberi 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa cha chikhulupiriro, Rahabi amene anali hule uja sanaphedwe limodzi ndi anthu osamvera, chifukwa iye analandira mwamtendere anthu amene anakafufuza za mzindawo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:31 Nsanja ya Olonda,11/1/2013, tsa. 131/15/1987, ptsa. 15-16
31 Chifukwa cha chikhulupiriro, Rahabi amene anali hule uja sanaphedwe limodzi ndi anthu osamvera, chifukwa iye analandira mwamtendere anthu amene anakafufuza za mzindawo.+