Aheberi 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mwa chikhulupiriro, Rahabi+ hule lija, sanawonongedwe limodzi ndi anthu amene anachita zinthu mosamvera, chifukwa iye analandira azondi mwamtendere.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:31 Nsanja ya Olonda,11/1/2013, tsa. 131/15/1987, ptsa. 15-16
31 Mwa chikhulupiriro, Rahabi+ hule lija, sanawonongedwe limodzi ndi anthu amene anachita zinthu mosamvera, chifukwa iye analandira azondi mwamtendere.+