Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mzindawu wapatulidwa kuti uwonongedwe,+ pakuti mzindawu limodzi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova. Rahabi+ yekha, hule uja, musamuphe. Mum’siye ndi moyo, iye pamodzi ndi onse amene ali naye m’nyumba mwake, chifukwa iye anabisa azondi amene tinawatuma.+

  • Mateyu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Salimoni anabereka Boazi, ndipo mayi ake anali Rahabi.+

      Boazi anabereka Obedi, ndipo mayi ake anali Rute.+

      Obedi anabereka Jese.+

  • Aheberi 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mwa chikhulupiriro, Rahabi+ hule lija, sanawonongedwe limodzi ndi anthu amene anachita zinthu mosamvera, chifukwa iye analandira azondi mwamtendere.+

  • Yakobo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 N’chimodzimodzinso ndi Rahabi.+ Kodi Rahabi hule lija, silinaonedwe ngati lolungama chifukwa cha ntchito zake, powalandira bwino azondi aja ndi kuwabweza kwawo powasonyeza njira ina?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena