Yoswa 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+ Oweruza 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anakhalabe ndi fuko la Yuda, moti linalanda dera lamapiri, koma silinathe kupitikitsa anthu okhala m’chigwa, chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta*+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.+ Oweruza 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno zinachitika kuti Aisiraeli anakhala amphamvu,+ ndipo anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ koma sanawachotseretu onse m’dzikolo.+ Salimo 106:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwowa sanawononge mitundu ina ya anthu,+Mmene Yehova anawauzira.+
13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+
19 Yehova anakhalabe ndi fuko la Yuda, moti linalanda dera lamapiri, koma silinathe kupitikitsa anthu okhala m’chigwa, chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta*+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.+
28 Ndiyeno zinachitika kuti Aisiraeli anakhala amphamvu,+ ndipo anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ koma sanawachotseretu onse m’dzikolo.+