Yoswa 15:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Amuna a fuko la Yuda analephera kuthamangitsa Ayebusi+ a ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi+ akukhalabe limodzi ndi Ayuda ku Yerusalemu mpaka lero. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:63 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
63 Amuna a fuko la Yuda analephera kuthamangitsa Ayebusi+ a ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi+ akukhalabe limodzi ndi Ayuda ku Yerusalemu mpaka lero.