Yoswa 15:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:63 Mawu a Mulungu, ptsa. 95-96
63 Ana a Yuda analephera kupitikitsa+ Ayebusi+ omwe anali kukhala ku Yerusalemu,+ moti Ayebusi akukhalabe limodzi ndi ana a Yuda ku Yerusalemu mpaka lero.