Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+

  • Yoswa 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+

  • Oweruza 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiyeno zinachitika kuti Aisiraeli anakhala amphamvu,+ ndipo anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ koma sanawachotseretu onse m’dzikolo.+

  • 1 Mafumu 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Palibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta, ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta, ndi a amuna ake okwera pamahatchi.+

  • 1 Mafumu 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza,+ koma Aisiraeli onse anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta n’kuthawira ku Yerusalemu.

  • 2 Mbiri 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma panalibe ana a Isiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo ogwira ntchito yake,+ chifukwa iwo anali ankhondo ake,+ atsogoleri a asilikali ake othandiza pamagaleta, atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta+ ndiponso a amuna ake okwera pamahatchi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena