Ekisodo 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+ Numeri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+ 2 Mbiri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+ 2 Mbiri 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu. Machitidwe 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo woyang’anira kachisi uja ananyamuka ndi alonda ake n’kukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa+ kuti anthu awaponya miyala.
4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+
10 Koma khamu lonselo linayamba kunena zoti liwaponye miyala.+ Kenako, ulemerero wa Yehova unaonekera kwa ana a Isiraeli onse pamwamba pa chihema chokumanako.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+
21 Pamapeto pake anthuwo anam’konzera chiwembu+ ndipo anam’ponya miyala+ pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu.
26 Pamenepo woyang’anira kachisi uja ananyamuka ndi alonda ake n’kukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa+ kuti anthu awaponya miyala.