2 Samueli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 1 Mafumu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+ 1 Mafumu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza,+ koma Aisiraeli onse anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta n’kuthawira ku Yerusalemu.
24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza,+ koma Aisiraeli onse anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta n’kuthawira ku Yerusalemu.