2 Samueli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 1 Mafumu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+
24 Adoramu+ anali kutsogolera anthu olembedwa ntchito yokakamiza, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
6 Ahisara anali woyang’anira banja lachifumu, ndipo Adoniramu,+ mwana wa Abada, anali woyang’anira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+