1 Mafumu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza,+ koma Aisiraeli onse anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta n’kuthawira ku Yerusalemu.
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza,+ koma Aisiraeli onse anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta n’kuthawira ku Yerusalemu.