Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu n’kudzigulitsa kwa inu,+ musam’gwiritse ntchito ngati kapolo.+ Yeremiya 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Isiraeli si mtumiki wanga+ komanso si kapolo wobadwira m’nyumba mwanga, si choncho kodi? Nanga n’chifukwa chiyani wafunkhidwa?
14 “‘Isiraeli si mtumiki wanga+ komanso si kapolo wobadwira m’nyumba mwanga, si choncho kodi? Nanga n’chifukwa chiyani wafunkhidwa?