Ekisodo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+ Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+
22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+