Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu n’kudzigulitsa kwa inu,+ musam’gwiritse ntchito ngati kapolo.+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”