5Hiramu+ mfumu ya ku Turo+ inatumiza atumiki+ ake kwa Solomo, pakuti inamva kuti iyeyo ndi amene anadzozedwa kulowa ufumu m’malo mwa bambo ake, popeza Hiramuyo ankamukonda Davide masiku ake onse.+
8 Choncho Hiramu anatumiza uthenga kwa Solomo, kuti: “Ndamva uthenga wanu. Ineyo ndichita zonse zimene mukufuna pa nkhani ya mitengo ya mkungudza ndiponso mitengo ina yofanana ndi mkungudza.+
14Ndiyeno Hiramu+ mfumu ya Turo+ anatumiza amithenga kwa Davide. Anatumizanso matabwa a mkungudza,+ anthu omanga makoma, ndi anthu a ntchito zamatabwa kuti akamangire Davide nyumba.+