Ezekieli 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti, ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kuwonongedwa kwako, kubuula kwa anthu ovulazidwa koopsa, ndi kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+ Ezekieli 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+
15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti, ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kuwonongedwa kwako, kubuula kwa anthu ovulazidwa koopsa, ndi kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+
3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+