Miyambo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+ Yesaya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+ Ezekieli 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo.+ Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘“Ndiwe chitsanzo changwiro. Uli ndi nzeru zochuluka+ ndipo ndiwe wokongola kwambiri.+
2 Mlendo akutamande, osati pakamwa pako. Munthu wochokera kudziko lina achite zimenezo, osati milomo yako.+
9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+
12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo.+ Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘“Ndiwe chitsanzo changwiro. Uli ndi nzeru zochuluka+ ndipo ndiwe wokongola kwambiri.+