Ezekieli 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+
3 Uimbire Turo kuti,“‘Iwe amene ukukhala polowera m’nyanja,+ mkazi wochita malonda ndi anthu okhala m’zilumba zambiri,+ tamvera zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine chiphadzuwa.’+