Ezekieli 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uimbire Turo kuti,‘Iwe amene ukukhala polowera mʼnyanja,Iwe amene ukuchita malonda ndi anthu amʼzilumba zambiri,Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine wokongola kwambiri.’+
3 Uimbire Turo kuti,‘Iwe amene ukukhala polowera mʼnyanja,Iwe amene ukuchita malonda ndi anthu amʼzilumba zambiri,Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe Turo wanena kuti, ‘Ine ndine wokongola kwambiri.’+