Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene waganiza zochita zimenezi,

      Kuti athetse kukongola kwa mzindawo komanso kunyada kwake,

      Kuti achititse manyazi anthu onse amene ankalemekezedwa padziko lonse lapansi.+

  • Ezekieli 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, uza mtsogoleri wa Turo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Chifukwa chakuti wadzikuza mumtima mwako,+ ukumanena kuti, ‘Ndine mulungu.

      Ndakhala pampando wachifumu wa mulungu pakatikati pa nyanja.’+

      Koma ndiwe munthu basi, osati mulungu,

      Ngakhale kuti mumtima mwako umadziona kuti ndiwe mulungu.

  • Ezekieli 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo. Uuze mfumuyo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:

      “Iwe unali chitsanzo changwiro,

      Unali ndi nzeru zochuluka+ ndiponso wokongola kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena