-
1 Mafumu 20:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho Ahabu anauza amithenga a Beni-hadadi kuti: “Mukauze mbuyanga mfumu kuti, ‘Zonse zimene munandiuza poyamba paja, ine mtumiki wanu ndichita. Koma zimene mwanena kachiwirizi, sindingathe kuchita.’” Atumiki a Beni-hadadi aja atamva zimenezi, ananyamuka kukapereka uthengawo kwa mfumu yawo.
-