Mateyu 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maonekedwe ake anali ngati a mphezi,+ ndipo zovala zake zinali zoyera mbee!+ Machitidwe 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo pamene onse amene anakhala m’bwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda anamuyang’anitsitsa,+ anaona kuti nkhope yake inali ngati nkhope ya mngelo.+
15 Ndipo pamene onse amene anakhala m’bwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda anamuyang’anitsitsa,+ anaona kuti nkhope yake inali ngati nkhope ya mngelo.+