Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chimodzimodzi inunso, panopa muli ndi chisoni. Koma ndidzakuonaninso ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzachititse kuti musiye kusangalala. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:22 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, tsa. 9
22 Chimodzimodzi inunso, panopa muli ndi chisoni. Koma ndidzakuonaninso ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzachititse kuti musiye kusangalala.