Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:22 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, tsa. 9
22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.