Yohane 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+ 1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+ 1 Akorinto 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake,+ Mwanayonso adzadziika pansi pa amene+ anaika zinthu zonse pansi pake, kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+ Afilipi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti iye anali ndi maonekedwe a Mulungu,+ kukhala wolingana ndi Mulungu sanakuganizirepo ngati chinthu choti angalande.+
17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+
28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake,+ Mwanayonso adzadziika pansi pa amene+ anaika zinthu zonse pansi pake, kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+
6 Ngakhale kuti iye anali ndi maonekedwe a Mulungu,+ kukhala wolingana ndi Mulungu sanakuganizirepo ngati chinthu choti angalande.+