Yohane 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwandimva ndikukuuzani kuti, Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu. Ngati munali kundikonda, mukanakondwera kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu+ kuposa ine.
28 Mwandimva ndikukuuzani kuti, Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu. Ngati munali kundikonda, mukanakondwera kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu+ kuposa ine.