-
1 Petulo 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ngakhale kuti Khristuyo simunamuonepo, mumamukonda. Ngakhale simukumuona panopa, mumamukhulupirira ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chodzaza tsaya,
-