1 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka, 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,2/1/1997, ptsa. 14-1912/1/1986, tsa. 26
8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,