Yohane 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anamufunsa kuti: “Kodi wakhulupirira chifukwa wandiona? Odala ndi amene amakhulupirira ngakhale sanaone.”+
29 Yesu anamufunsa kuti: “Kodi wakhulupirira chifukwa wandiona? Odala ndi amene amakhulupirira ngakhale sanaone.”+