2 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 pakuti tikuyenda mwa chikhulupiriro, osati mwa zooneka ndi maso.+ 1 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,
8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,