Aroma 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti tinapulumutsidwa tili ndi chiyembekezo chimenechi,+ koma chimene chikuyembekezedwa chikaoneka sichikhalanso choyembekezedwa, chifukwa munthu akaona chinthu chimene anali kuchiyembekezera, kodi amachiyembekezanso? 2 Akorinto 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 pamene tikuika maso athu pa zinthu zosaoneka, osati pa zooneka.+ Pakuti zooneka n’zakanthawi,+ koma zosaoneka n’zamuyaya.+
24 Pakuti tinapulumutsidwa tili ndi chiyembekezo chimenechi,+ koma chimene chikuyembekezedwa chikaoneka sichikhalanso choyembekezedwa, chifukwa munthu akaona chinthu chimene anali kuchiyembekezera, kodi amachiyembekezanso?
18 pamene tikuika maso athu pa zinthu zosaoneka, osati pa zooneka.+ Pakuti zooneka n’zakanthawi,+ koma zosaoneka n’zamuyaya.+