Aroma 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndiye amene anafa, zoonadi, amenetu anaukitsidwa kwa akufa. Iye ali kudzanja lamanja+ la Mulungu, ndipo amatilankhulira mochonderera kwa Mulunguyo.+ 2 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 pakuti tikuyenda mwa chikhulupiriro, osati mwa zooneka ndi maso.+ Aheberi 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chikhulupiriro+ ndicho chiyembekezo chotsimikizika cha zinthu zoyembekezeredwa,+ umboni wooneka wa zinthu zenizeni, ngakhale kuti n’zosaoneka.+
34 Ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndiye amene anafa, zoonadi, amenetu anaukitsidwa kwa akufa. Iye ali kudzanja lamanja+ la Mulungu, ndipo amatilankhulira mochonderera kwa Mulunguyo.+
11 Chikhulupiriro+ ndicho chiyembekezo chotsimikizika cha zinthu zoyembekezeredwa,+ umboni wooneka wa zinthu zenizeni, ngakhale kuti n’zosaoneka.+