Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Luka 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ndinu odala anthu akamadana nanu,+ kukusalani, kukunyozani ndi kukana+ dzina lanu n’kumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu. Yakobo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abale anga, sangalalani pamene mukukumana ndi mayesero osiyanasiyana,+ 1 Petulo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+
22 “Ndinu odala anthu akamadana nanu,+ kukusalani, kukunyozani ndi kukana+ dzina lanu n’kumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu.
14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+